
Inde Phiri!; Ndine Takondwa, katswiri wopanga ma webusayiti Otsogola, ndimapanga masamba a intanent okongola, othamanga, ndi osavuta kugwiritsa ntchito; omwe amakhala oyenera ndi zomwe inu mwafuna.
Ngati muli ndi mafunso aliwonse, kapena mukufuna kumwa ☕️ ndi ine, chonde muzikhala omasuka kundilankhula.
Tiyeni timwe khofi ☕️